August 01, 2024
BURN Manufacturing Co. is implementing carbon project activities in Malawi under the Gold Standard Programme of Activities (PoA) ‘ECOA_BURN multi-country Clean Cooking Programme’. On the 9th to 15th July 2024, BURN invited stakeholders to the Local Stakeholder (LSC) meetings where the project and its impacts were introduced, and comments and feedback sought from participants.
This is to invite you our esteemed stakeholder to the Gold Standard Stakeholder Feedback Round of the project (SFR). Please find attached the Local Stakeholder meeting summary report in English and Chichewa for your review. Kindly let us know if you have any further comments or feedback.
These documents can also be found at our country project consultant office in Blantyre Malawi, and you can pay him a visit at Malawi Blood Transfusion Service offices in Blantyre along Victoria Avenue opposite Victoria Garden,or call 0999551985.
Please send us your feedback by 1st of September 2024 to BURN Project manager via email stanley.kiriungi@burnmfg.com or sally.gakii@burnmfg.com
Kampani ya BURN yayambitsa polojeketi kuno ku Malawi pansi pa zochitika za pologalamu ya ‘ECOA_BURN multi-country Clean Cooking Programme’. Pa 9th mpaka 15th July 2024, BURN inaitanitsa msokhano wa anthu okhuzidwa mu polojeketi imeneyi komwe inalongosola cholinga ndi zotsatira za polojeketi komanso kumva mafunso ndi ndemanga kwa onse oitanidwa.
Tikukupephani inu okondedwa anthu kuti mutipatse ndemanga zanu pa zotsatira za msokhanowu. Taika Lipoti mwachidule la msokhano wa anthu okhudzudwa mu chiyakhulo cha Chichewa ndi chingerezi kuti muliwunikire. Chonde tiuzeni ngati muli ndi zoonjezera zina kapena ndemanga. Malipoti amanewa akupezekanso kwa nthumwi yathu yomwe imapezeka ku Blantyre Malawi.
Mungathe kukumana nayo nthumwi imeneyi ku maofesi a Malawi Blood Transfusion Service ku Blantyre
mphepete mwa nseu wa Victoria Avenue moyan’ganana ndi Victoria Garden, kapena Kuimba foni pa 0999551985
"Chonde tumizani maganizo anu pofika pa 1st of September 2024 kwa BURN Project Manager kudzera pa imelo stanley.kiriungi@burnmfg.com or sally.gakii@burnmfg.com